Photo Gallery

Epifania-2017 Radio Maria Malawi Volunteer Newly Open Grotto Opening Local Mariathon and Grotto 2016 Opening Local Mariathon and Grotto Holy Mass Opening of 2016 Local Mariathon and Grotto Radio Maria Malawi Volunteer Praying Rosary Radio Maria World Family Meeting Directror RadioMaria Malawi

Programme Schedule

Contact us

Radio Maria Malawi
P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 605 /607 /608 /626/627
Fax. (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

WFRM Newsletter

Welcome

RADIO MARIA is a broadcasting initiative, which was started in Italy by a group of Catholics, both priests and lay people. It aims at spreading the Good News of Jesus Christ to all people of good will. The radio is not commercially funded through advertisement, but lives solely by means of the generous donations of its listeners and the contributions of its volunteers.

On Radio Maria Malawi website you can listen to our live broadcast by clicking on the Live & Direct icon on the right hand side. You can also listen to recorded Ulaliki and music by going to the Media menu.

Please take the time to make a small donation to help us evangelise to poor souls. May God bless you all.

Nkhani ndi Zochitika

 • 20 February 2017
  Episkopi wa dayosizi ya mpingo wa katolika ya Mangochi Ambuye Montfort Stima apempha anthu omwe akuthandizika ndi bungwe lowoona za chitukuko mu mpingowu la CADECOMkuti akhale odziyimira pawokha kudzera mu ntchito zomwe bungweli likugwira. Ambuye Stima alankhula izi loweruka ku parishi ya Mpiri mu dayosiziyi pa mwambo wokhazikitsa ndondomeko ya ...
 • 19 February 2017
  Kuletsa kwa galimoto za matola m’boma la Mangochi ati kwathandiza kubweretsa bata pa nsewu komanso kuchepetsa ngozi za pansewu m’bomalo. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo inspector Rodrick Maida wauza Radio Maria Malawi kuti chikhazikitsireni ndondomeko  yoletsa galimoto za matola m’bomali, ndondomeko yomwe inakhazikitsidwa pa 20 November ...
 • 19 February 2017
  Mwana wina wa chaka chimodzi wafa atamira m’madzi m’boma la Mangochi. Izi zachitika m’mudzi mwa Chipoka mfumu yaikulu Mponda m’bomalo. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Inspector Rodrick Maida wauza Radio Maria Malawi kuti patsikuli mwanayu amakwawa mozungulira nyumbayi koma makolo ake samadziwa mayendedwe a mwana wawo kufikira pamene ...
 • 19 February 2017
  Arkidayosizi ya mpingo wa katolika ya Blantyre yalimbikitsa akhristu a mpingowu kuti abzale mitengo ngati njira imodzi yobwezeretsa chilengedwe mdziko muno. Vicar General wa arkidayosiziyi bambo Boniface Tamani alankhula izi pa mwambo wokhazikitsa ntchito yobzala mitengo yomwe ikutsogoleredwa ndi bungwe la amai achikatolika la Catholic Women ...
 • 18 February 2017
  Bungwe lalikulu loyang’anira akatswiri omenya nkhonya mdziko muno la Malawi Professional Boxing Control Board lati ndi lokhumudwa kaamba ka mchitidwe wa omenya nkhonya ena omwe akugwira ntchito ndi mabungwe awiri osiyana zomwe ati ndi kuphwanya malamulo a masewerawa pa dziko lonse. Mkulu wofalitsa nkhani ku bungweli a Frank Chibisa ndi omwe anena ...

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices