Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Papa Francisco Ayendera Dziko la Portugal 

 

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wanyamuka kupita mdera la Fatima mdziko la Portugal komwe akakhale nawo pa chikondwelero chakuti padutsa zaka 100 chiwonekereni amayi Maria ku malowa.

Malipoti a wailesi ya Vatican ati pa ulendowu Papa akuyembekezekanso kukatchula oyera awiri mwa ana omwe amayi Maria anawaonekera.

Alendo oposera 1 miliyoni ochokera mmadera osiyanasiyana akuyembekezeka kukakhala nawo pa mwambowu ndipo padakali pano dziko la Portugal lakhwimitsa chitetezo mmalire onse a dzikolo.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices