Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Bambo Wina Adzipha Ku Nkhotakota Pa Nkhani Za M’banja. 

 

Bambo wina wa zaka 25 zakubadwa m’boma la Nkhotakota wadzipha podzimangilira atamvetsedwa kuti mkazi wake akuchita chibwenzi cha nseli ndi mwamuna wina.

Malingana ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo  Paul Malimwe,  malemu-yi Masauko Makiyi anadzipha pa 2 August kamba ka nkhani-yi.

Padakalipano apolisi ati apitiliza kufufuza mpaka atapeza zotsatira zeni zeni za  imfa ya malemuyi.

Malemuyi Masauko Makiyi  amachokera m’mudzi mwa Mvula m’dera la mfumu yayikulu Mphonde m’boma lomwelo la Nkhotakota. 

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices