Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Mphunzitsi wamkulu Afa Pozimangilira. 

 

Mphunzitsia wamkulu wa pa sukulu ya pulaimale m’boma la Dowa wazipha pozimangilira kudenga la nyumba yake.

Malinga ndi ofalitsa za apolisi m’bomalo Sergent Richard Kaponda wati mphunzitsiyu ndi Briay Mghogho ndipo amagira ntchito yake pa sukulu ya pulaimale Mpalamkwali m’bomalo.

Malinga ndi malipoti ati bamboyu akumuganizira kuti wadzipha kaamba kowawidwwa mtima potsatira kuvulala kwa miyendo yake yomwe anavulala pa ngozi ya pa msewumasiku apitawo.

Malemuyu amachokera m’mudzi wa Masi kwa mfumu yaikulu Msakambewa m’boma la Dowa.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices