Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Ayamikira Anthu Chifukwa Chopereka Magazi 

 

Bungwe lopereka magazi la MALAWI BLOOD TRANSFUNSION SERVICE (MBTS) layamikira anthu  a m’boma la Ntcheu kaamba kodzipereka pantchito yopereka magazi pamene bungweli limagwira ntchito yotolera magazi m’madela ena m’bomali

Malingana ndi m’kulu woyang’anira ntchito yopereka magazi m’bomali a ZIONE CHIMALIZENI, Iwo ati kuonetsa chidwi pa ntchito yopereka magazi zimasonyeza kuti munthu akumvetsa bwino cholinga cha bungweli.

Pamenepa a Chimalizeni apempha anthu mdziko muno kuti adzikonda kupereka magazi  kuti dziko lino lipulumutse miyoyo ya nthu omwe amasowa magazi mzipatala zosiyanasiayana. 

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices