Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Mpingo Wa Anglican Udzipereka Pa Ntchito Zokweza Achinyamata. 

 

Dayosizi ya mpingo wa Anglican ya Uppershire yati ipitiliza kulimbikitsa ntchito za achinyamata mu mpingo-wu.

Episikopi wa mpingo-wu mu dayosizi-yi , Ambuye Brighton Vitta Malasa , ndi omwe anena izi pakutha pa mwambo wa mpikisano wamayimbidwe umene anakhadzikitsa pakati pa makwaya a mpingo-wu mu dayosizi-yi .

Mpikitsanowu unali wandalama zokwanira 1 million kwacha ndipo unachitika pa 14 October 2017 ku Likwenu Parish ku Malosa m’boma la Zomba.

Malingana ndi zotsatira za mpikitsano wa mayimbidwewu mu dayosizi ya mpingo wa Anglican ya Uppershire , kwaya ya mposa kuchokera m’boma la Machinga ndi yomwe inakhala nambala 1 , ndipo yalandira ndalama zokwanira 350 thousand , ndalama ndi mphoto zina  zapitanso ku makwaya ena omwe anachita bwino mu mpikitsano-wu.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices