Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Anamwino Adzipereka Pogwira Ntchito Zachifundo Pakati Pa Odwala Mdziko Muno 

 

Anamwino m’dziko muno alonjeza kuti apitiliza ntchito yosamalira bwino odwala mzipatala zonse mdziko muno.

 

President wa gulu la anamwino kudzera pa tsamba la whatsap a blessings ganti , ndi amene wanena izi loweluka , pamene guluri limakachezera odwala pachipatala cha boma , ku mulanje.

 

Mayi Genti ati nthawi yakwana yoti anamwino adzidziwika ndi ntchito zabwino osati monga anthu akhala akunenera kuti ma nesi ena amakhala akuchitira nnkhanza odwala.

 

Iwo ati bungwe lawo lipitiiza kulimbikitsa makhalidwe abwino ndi okonda kulimbikitsa ntchito za chifundo pakati pa odwala mdziko muno.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices