Photo Gallery

Radio Maria Malawi Choir Festival 2017 Fundraising Big Walk Opening of 2016 Local Mariathon and Grotto Minister of Information and Civic Education Visiting Radio Maria Malawi Radio Maria  World Family Meeting Group Photo-Staff and Volunteers Radio Maria Malawi with Minister of Information Bicycle Fund Raising Ride-For Radio Maria Malawi

Programme Schedule

Contact us

Radio Maria Malawi
P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 605 /607 /608 /626/627
Fax. (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Apempha Aphungu Akhale Odzetsa Mtendere 

 

Aphungu akunyumba yamalamulo,awapempha kuti akhale anthu odzetsa mtendere pamene akutumikira anthu mmadera osiyanasiyana mdziko muno.

Wapampando wa amai mchipani cholamula cha Democratic Progressive DPP mai Patricia Kaliati omwenso ndi phungu wakunyumba ya malamulo mdera la kumvuma m’boma la Mulanje, apereka pempholi lero pamwambo okhazikitsa bungwe la aphungu akunyumba ya malamulo lowona za mtendere mdziko muno,lomwe likutchedwa International Association of Parliamentarians for Peace Caucus.

Mai Kaliati, omwenso ndi wapampando wa bungweli,ati nthawi yakwana yoti aphungu akunyumba yamalamulo, akhale zida zodzetsa mtendere makanso poyika patsogolo Mulungu.Iwo ati bungweli lidakhazikitsidwa kale m’maiko ena, ndipo dziko lino, lawonanso kuti nkofunika kukhala nalo kuno ku Malawi monga zilili mmaiko ena.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices