Photo Gallery

Radio Maria Malawi Choir Festival 2017 Fundraising Big Walk Opening of 2016 Local Mariathon and Grotto Minister of Information and Civic Education Visiting Radio Maria Malawi Radio Maria  World Family Meeting Group Photo-Staff and Volunteers Radio Maria Malawi with Minister of Information Bicycle Fund Raising Ride-For Radio Maria Malawi

Programme Schedule

Contact us

Radio Maria Malawi
P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 605 /607 /608 /626/627
Fax. (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Bwanamkubwa wa Balaka Apempha Mgwirizano 

 

Khonsolo ya boma la Balaka yapempha kuti pakhale ubale wabwino pakati pa adindo ndi makomiti a za chitukuko m’bomalo.

Bwanamkubwa wa bomalo, Rodrick Mateauma ndi yemwe wanena izi potsatira mphekesera yomwe yakhala ikumveka yoti  magulu awiriwa sakulumikizana pa ntchito  zachitukuko m’bomalo.

Iye watinso zikuonetsa kuti vuto lonseli likuchitika kaamba koti makhansala ena sakuzindikirabe udindo wawo ndi zoyenera kuchita izi ndi zimene zikuchitisa kuti makomiti achitukuko ndi makhansalawa adzisemphana pakagwiridwe ka ntchito.

Polankhulapo  m’modzi mwa makhansala a m’bomalo Peterson Bwanali  wathirirapo ndemanga  kuti  ubale wa magulu awiriwa wakhala usakuyenda bwino m’bomalo.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices