Photo Gallery

Radio Maria Malawi Choir Festival 2017 Fundraising Big Walk Opening of 2016 Local Mariathon and Grotto Minister of Information and Civic Education Visiting Radio Maria Malawi Radio Maria  World Family Meeting Group Photo-Staff and Volunteers Radio Maria Malawi with Minister of Information Bicycle Fund Raising Ride-For Radio Maria Malawi

Programme Schedule

Contact us

Radio Maria Malawi
P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 605 /607 /608 /626/627
Fax. (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Chipani cha MCP Sichikudziwapo Kanthu pa “Antchito” 

 

Chipani cha Malawi Congress(MCP) chati sichikudziwapo kanthu kwa achinyamata omwe akuti anabwera ku likulu la chipanichi m’chigawo cha ku m’mwera kudzafuna malipiro awo a ntchito.

Wapampando wa chipani mchigawochi a Peter Simbi ndiye yemwe wanena pa msonkhano wachipanichi umene unachitikira mu m’dzinda wa Blantyre.

Iwo ati pa chisankho chachibweleza chomwe chinachitika m’dziko muno chipani chawo sichinalembe ntchito achinyamata kuti adzayanganire ntchito zochitika pa chisankhochi koma kuti onse omwe anagwira ntchito-yi anali anthu odzipeleka ochokera m’madera momwe mukanchitikira chisankhochi.

Chipanichi chanena izi kamba koti pakhala pakumveka zoti achinyamata achipanichi pa 8 mwezi uno anavala kakaka achipanichi ndi kupita ku maofesi ake mu m’dzinda-wu ati kukakumbutsa ndalala za malipiro awo okhudzana ndi ntchito yomwe anagwira pa nthawi ya sizankhozi.

Naye phungu wa chipanichi m’dera laNsanje Lalanjea Lawrence Sitoloanati nawo akudabwa kwambiri ndi nkhaniyi kamba koti chipani chawo chimakhala ndi dongosolo labwino lochitira zinthu.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices