Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Mafumu Ati Adzigwira Ntchito Limodzi ndi Boma 

 

Mfumu yayikulu Mbenje ya m’boma la Nsanje yalangiza mafumu m’dziko muno kuti adzigwira ntchito limodzi ndi boma lomwe likulamula ndi cholinga chofuna kulimbikitsa ntchito za chitukuko m’dziko lino.

Mfumuyi imalankhula izi pa mwambo wokweza Nyakwawa Kadamila kukhala a Group Village Headman ya mdela lake. Iwo ati mafumu akuyenera kumadzipeleka pa ntchito zotumikira boma lomwe likulamula pofuna kupititsa patsogolo ntchito yotukula dziko lino. 

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices