Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Mphunzitsi Azipha Pozimangilira M’boma la Dedza 

 

Bambo wina wa zaka 47zakubadwawadzipha podzimangilira m’boma la Dedza.

Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Edward Kabango, bambo-yu ndi Ives Kumankhamba ndipo anali mphunzitsi pa sukulu ya pulayimale ya Buam’bomalo.

Malemuyi akuti wadzipha mkazi wake anali kumudzi komwe amakazonda odwala. Padakalipano  gwero la imfa ya mkulu-yi silikudziwika.

Malemu Ivesi Kumankhamba amachokera m’mudzi mwa Fosa kwa mfumu yaikulu Kachere m’boma lomwelo la Dedza.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices