Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Kabwerebwere Alamulidwa Zaka 9 ku Ndende 

 

Bambo wina wa zaka 32 zakubadwa amulamula kuti akakhale ku ndende ndi kukagwira ntchito ya kalavulagaga kwa zaka zisanu kaamba kothyola shop ndi kuba katundu wa ndalama za nkhaninkhani.

Wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za apolisi m’boma la Mangochi, Sergeant Amina Daudi wauza Radio Maria Malawi kuti mkuluyu, Emmanuel Joseph anathyola shop ya m’mwenye ndi kuba 500 thousand kwacha ndi mafoni 32ndipo katundu yenseyu ndi wa ndalama zokwana 2.1 million kwacha.

Mkuluyi walandira chilangochi pamenenso sabata yatha amulamula kuti akakhale ku ndende kwa zaka zinayi kaamba ka mulandu wa ngati womwewu.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices