Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Afa Atawombedwa ndi Galimoto ku Ntchisi 

 

Bambo wina wafa ataombedwa ndi njinga ya moto m’boma la Ntchisi.

Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo, Sergeant Gladson Mbumpha wati a Bruno Malithano a zaka 38zakubadwa anakwezana njingayo yomwe ndi yosalembetsedwa ndi anzawo ena awiri ndipo atafika pa Kalumo anawomba mkulu wina yemwe amayenda mbali mwa nsewu-wo yemwenso anali ataledzera.

Kutsatira ngoziyi mkuluyu yemwe sakudziwika dzina lake anakafera ku chipatala cha boma la Ntchisi kaamba koti anavulala kwambiri m’mutu.

Pakadali pano apolisi m’bomalo akusakasaka anthu omwe anawomba mkuluyu kaamba koti zitachitika izi anathawa.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices