Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Amsembe A Ku Chikwawa Azamitsa Moyo Wawo Wa Uzimu. 

 

Amsembe a mpingo wakatolika mu dayosizi ya Chikwawa anakumana malo amodzi ndi kuzamitsa moyo wawo wa uzimu ku dzera mu mbindikiro wawo umene anali nawo kuyambira pa  6 august ndi kutha pa 11 mwezi uno.

M’bindikiro unachitira ku St John of the Cross Spirituality Center Ku Nyungwi m’boma laChiradzulu mu arch dayosizi ya Blantyre.

Bambo Joseph Kimu, omwe ndi a director a Radio Maria Malawi, ndi omwe anatsogolera amsembe-wa pa m’bindikiro-wu.  

Polankhula kumapeto a mbindikirowu bambo Henry Biliwita  omwe ndi a bambo mfumu a parish ya Bangula m’boma la Nsanje mogwilizana ndi bambo Martin Hanock a parish ya Konza Alendo m’boma la Thyolo mu dayosizi-yi anati apindula koposa ndi maphunziro ozama omwe alandira mkatikati mwa m’bindikiro

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices