Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Anthu 20 Afa Boti Litamira Mdziko la Myanmar 

 

Anthumakumi awiri (20)afa boti lomwe anakwera litaombana ndi  linzake ndi kumira mu m’tsinje wina m’dziko la Myanmar.

Malingana ndi malipoti a News 24 anthu amene anali mu botili ndi oti anali akuchokera ku mwambo wa ukwati ku dela lina ndipo onse analipo 60.

Malipoti-wo ati mwa anthu omwe afawo 16ndi amayi ndipo anayiwo ndi amuna.

Ngozi za pamadzi akuti zimakonda kuchitikachitika mdzikomo kamba koti anthu ambri amakonda kugwilitsa ntchito maulendo a pamadzi.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices