Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Anthu 20,000 a Mdziko la Myanmar Athawira Mdziko la China 

 

Anthu othawa kwawo oposa 20 thousand a mdziko la Myanmar ati alowa mdziko la China pothawa zamtopola zomwe zinabuka kummwera cha kummawa kwa maiko a mchigawo cha Asia.

Malinga ndi malipoti padakali pano anthuwa akupatsidwa thandizo la zosowa zawo mongoyembekezera pofuna kupewa nkhondoyi.

Padakali pano dziko la China lapempha maiko omwe akukhudzidwa ndi zamtopolazi kuti ayambe asiya ndipo akhale pansi ndi kukambirana.

Malipoti a NEWS 24 ati magulu omwe akukhudzidwa ndi za mtopolazi ndi asilikali a zikhalidwe zinayi za mchigawochi.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices