Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Anthu makumi Asanu Amira pa Nyanja ya Meditteranean 

 

Bwato lomwe linanyamula anthu oposa makumi asanu akuliganizira kuti lamira pa nyanja yaikulu ya Meditteranean mdziko la Morocco.

Malinga ndi malipoti a bbc magulu opulumutsa anthu pa ngozi za pa madzi ati mwa anthuwa akwanitsa kupulumutsa anthu awiri omwe ndi a zaka za pakati pa 17 ndi 25 ndipo padakali pano akulandira thandizo ku chipatala cha Almeria kummwera kwa dziko la Spain.

Malipoti ati bwatoli lomwe limapita mdziko la Spain lakhala likuyenda mosayenera kwa masiku angapo chinyamukire mdziko la Morocco.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices