Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Apempha Mafumu Kusunga Chikhalidwe  

 

Mfumu yayikulu ya mtundu wa Alhomwe mdziko muno yapempha ndikulangiza mafumu a mtunduwu kuti alimbikitse kusunga chikhalidwe chomwe ndi maziko a chikondi pakati pawo.  

Paramount Chief  Ngolongoliwa ndiwomwe alankhula izi pamene amakumana ndi mafumu ang’ono ang’ono  a mtunduwu ochokera mboma la Zomba.

Ngolongoliwa wati ngati mafumu atalimbikitsa chikondi  pakati pa anthu awo zingathandize kupititsa pa tsongolo ntchito za chitukuko mmadera awo. 

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices