Make a Donation

 
  
  Donate Online
 
    Bank
 
   
     Phone

       

 

Direct debit payment

 

Kodi mukudziwa kuti mukhoza kuthandiza Radio Maria Malawi potumiza ma unitsi a phone? Maunisti a phone amatithandiza kuulutsa mapologalamu osiyanasiyana.

Inu amene mumagwiritsa ntchito Airtel, TNM kapena MTL mukhoza kutumiza maunisti kuthandiza Radio Maria pogwiritsa njira ija imene imatchedwa ME2U.

- Nayi nambala ya Airtel kumene mutha kutumiza maunisti anu 0991-805-056 komanso 0999-805-056

- Nayi nambala ya TNM kumene mutha kutumiza maunisti anu 0884-594-554

-Nayi nambala ya MTL kumene mutha kutumiza maunitsi anu 0111-955-533

Mulungu aonjezere pamene mudzatapa ncholinga chofuna kuthandiza Radio Maria.

 

ME 2 U DONATIONS:

AIRTEL: 0991 805 056

           :0999 805 056

TNM    : 0884 594554

MTL    :0111 955 533

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices