Photo Gallery

Radio Maria Malawi Choir Festival 2017 Fundraising Big Walk Opening of 2016 Local Mariathon and Grotto Minister of Information and Civic Education Visiting Radio Maria Malawi Radio Maria  World Family Meeting Group Photo-Staff and Volunteers Radio Maria Malawi with Minister of Information Bicycle Fund Raising Ride-For Radio Maria Malawi

Programme Schedule

Contact us

Radio Maria Malawi
P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 605 /607 /608 /626/627
Fax. (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Welcome

RADIO MARIA is a broadcasting initiative, which was started in Italy by a group of Catholics, both priests and lay people. It aims at spreading the Good News of Jesus Christ to all people of good will. The radio is not commercially funded through advertisement, but lives solely by means of the generous donations of its listeners and the contributions of its volunteers.

On Radio Maria Malawi website you can listen to our live broadcast by clicking on the Live & Direct icon on the right hand side. You can also listen to recorded Ulaliki and music by going to the Media menu.

Please take the time to make a small donation to help us evangelise to poor souls. May God bless you all.

Nkhani ndi Zochitika

  • 17 November 2017
    Apolisi m’boma la Ntchisi akufunafuna oyendetsa galimoto wina yemwe wapha munthu atamuwomba ndi galimoto ndikuthawa.       Malinga ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergeant Gladson M’bumpha, ngoziyo, yachitika lachitatu pa 15 November, pomwe galimotolo, lomwe pano silidadziwike limachokera mbali ya Nkhotakota kupita ku Kasungu komwe ...
  • 16 November 2017
    Maepiskopi a mpingo wa katolika mmaiko a Africa ndi ku Ulaya, ayamikira mfundo zomwe bungwe la mgwirizano wa maiko a mu Africa ndi ulaya, agwirizana kuti adzakambirane, pa msonkhano wawo wachisanu omwe uchitike chaka chino ku Albidjan mdziko la Ivory Coast. Maepiskopiwa ati ndi okondwa, maka chifukwa cha mfundo yokhudza achinyamata yomwe ili ...
  • 16 November 2017
    Bungwe la mgwirizano wa maiko a mu Africa la African Union (AU), lati zomwe achita asilikali a dziko la Zimbabwe potenga udindo oyendetsa boma, ndi chimodzimodzi kulanda boma ngakhale asilikaliwo akutsutsa izi. Wapampando wa bungweli a Alpha Conde, yemwenso ndi mtsogoleri wadziko la Guinea, ndi yemwe wanena izi, ndipo walamula kuti zonse ...

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices