Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Mfumu Chikumbu Idana Ndi Zoti Atsikana Azithandizira Miyambo Ya Chikwati. 

 

Mfumu yayikulu chikumbu ya m’boma la Mulanje yati sikugwilizana ndi m’chitidwe woti ana achitsikana azigwilitsidwa ntchito zovina pa miyambo ya zikwati kukhala ma (Dancing Queens).

Mfumuyi yalankhula izi pofotokozera mtolankhani wathu amene amafuna kumva zina mwa mapulani omwe mfumuyi ili nawo pa nkhani zotukula maphunziro a atsikana m’bomalo.

Mfumuyi yati itafufuza yapeza kuti m’chitidwe wolora atsikana kumavina mzikwati ngati ma Dancing Queens ndi umene ukukolezera zoti atsikana azikwati-wa msanga kamba koti  zikumawapangitsa kuti azikhumbira zolowa mbanja adakali achichepere. 

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices