Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Papa Wati Akhristu Kuyenera Kukahala Achikondi Ndi Olimba Pa Chikhulupiliro  

 

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco wapempha akhristu kuti azikhala achikondi ndi olimba pa chikhulupiliro chawo.

Papa walankhula izi pomwe amathililapo ndemanga pa zakutchulidwa kwa akhristu 35 a mpingo-wu kuti ndi oyera.

akhristu-wa avomelezedwa pa 15 october ndi mpingo-wu kuti ndi oyera mu mpingo, pa mwambo waukulu , umene unachitikira pa bwalo La St Peters Square , ku likulu la mpingo-wu ku Vatican.

Oyera atsopano mu mpingowu , achokera m’mayiko a Brazil,  Mexico, Spain ndinso Italy.  mwa oyera atsopano-wa muli amsembe awiri.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices