Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Zigawenga 36 za Islamic State Zaphedwa 

 

Zigawenga 36 za gulu la zauchifwamba la Islamic State ISzafa komanso malo omwe zimakhala awonongedwa mdziko la Afghanstan potsatira bomba lomwe linaponyedwa ndi asilikali a mdziko la America.

Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC bombali lomwe linali lalikulu pa mabomba omwe asilikaliwa amagwiritsa ntchito, linaponyedwa pa malo omwe zigawengazi zimakhala mdera la Nangarhar ndipo ati palibe munthu wamba yemwe wavulala.

Pulezidenti wakale wa dziko la Afghanstan ati wadzudzula mchitidwewu kuti ndi wosayenera ku dzikolo.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices